Quantcast
Channel: Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 46483

Tonse yakanika kutumikira a Malawi, iyambe kupakila, chatero chipani cha DPP

$
0
0

Chipani chotsutsa boma cha DPP chati ulamuliro wa mgwirizano wa Tonse uyambe kuchotsera masiku ake okhala m’boma kaamba koti alephera kutumikira a Malawi. Gavanala wachipanichi mchigawo chakumvuma Sheikh Imran Ntenje wati umoyo wa nzika ukupitilira kukhala wa umphawi mu zaka zinayi zomwe utsogoleriwu walamulira dziko lino. Sheikh Ntenje wati katundu ofunikira monga chimanga, sugar komanso […]

The post Tonse yakanika kutumikira a Malawi, iyambe kupakila, chatero chipani cha DPP appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.

Viewing all articles
Browse latest Browse all 46483

Latest Images

Trending Articles



Latest Images

<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>