Quantcast
Channel: Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 46064

Chakwera adzudzula boma la USA poletsa a Malawi ena kupita ku USA: ‘Akuzengedwa milandu, khoti silidawapezebe olakwa.’

$
0
0

President Lazarus Chakwera wati ndiodabwa ndi ganizo la dziko la America loletsa mzika zinayi zadzikolino kupita mdzikoli ati kamba kokhudzidwa ndi mchitidwe wa ziphuphu ndi katangale. Mtsogoleriyu wati ndizodabwitsa kuti dziko la America likupeleka chilango kwa anthu omwe bwalo lamilandu kuno silidawapeze olakwa chikhalirecho ku America ko kumachitika umbava ndi umbanda ochuluka kuposa ku Malawi […]

The post Chakwera adzudzula boma la USA poletsa a Malawi ena kupita ku USA: ‘Akuzengedwa milandu, khoti silidawapezebe olakwa.’ appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.

Viewing all articles
Browse latest Browse all 46064

Trending Articles



<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>